-
Nahumu 1:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
Ndidzachotsa zifaniziro zosema ndi zifaniziro zachitsulo mʼnyumba* za milungu yako.
Ndidzakukonzera manda chifukwa uli ngati chinthu chonyansa.’
-