15 Taonani mapazi a munthu yemwe akuyenda pamwamba pa mapiri pobweretsa uthenga wabwino.
Iye akulengeza za mtendere.+
Iwe Yuda, chita zikondwerero zako.+ Kwaniritsa zimene walonjeza,
Chifukwa munthu aliyense wopanda pake sadzadutsa pakati pako.
Munthu wopanda pakeyo adzaphedwa.”