Nahumu 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Womwaza wabwera kudzalimbana nawe.*+ Teteza malo amene ali ndi mpanda wolimba kwambiri. Londera njira yako. Konzekera kumenya nkhondo* ndipo sonkhanitsa mphamvu zako zonse.
2 Womwaza wabwera kudzalimbana nawe.*+ Teteza malo amene ali ndi mpanda wolimba kwambiri. Londera njira yako. Konzekera kumenya nkhondo* ndipo sonkhanitsa mphamvu zako zonse.