-
Nahumu 2:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Magaleta awo ankhondo akuthamanga kwambiri mʼmisewu.
Iwo akuthamanga uku ndi uku mʼmabwalo a mzinda.
Akuwala ngati matochi komanso kungʼanima ngati mphezi.
-