-
Nahumu 2:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Tengani siliva wawo, tengani golide,
Iwo ali ndi chuma chankhaninkhani.
Ali ndi zinthu zosiyanasiyana zamtengo wapatali.
-