-
Nahumu 3:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Tsoka mzinda wokhetsa magazi!
Mzindawo wadzaza ndi chinyengo ndi zauchifwamba,
Ndipo nthawi zonse umatenga zinthu za anthu omwe wagonjetsa.
-