Nahumu 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kukumveka kulira kwa mikwapulo ndiponso phokoso la mawilo,Mgugu wa mahatchi* ndi kuthamanga kwa magaleta.
2 Kukumveka kulira kwa mikwapulo ndiponso phokoso la mawilo,Mgugu wa mahatchi* ndi kuthamanga kwa magaleta.