-
Nahumu 3:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Zili choncho chifukwa cha kuchuluka kwa zochita zake zauhule.
Iye ndi mkazi wokongola mochititsa kaso ndiponso waluso lamatsenga.
Ndipo amakopa mitundu ya anthu ndi uhule wake komanso mabanja ndi zochita zake zamatsenga.
-