Nahumu 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti: “Taona! Ine ndikukuukira,*+Ndipo ndidzakuvula zovala zako nʼkukuphimba nazo kumaso.Ndidzachititsa kuti mitundu ya anthu ione maliseche ako,Ndipo maufumu adzaona kuti wachititsidwa manyazi.
5 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti: “Taona! Ine ndikukuukira,*+Ndipo ndidzakuvula zovala zako nʼkukuphimba nazo kumaso.Ndidzachititsa kuti mitundu ya anthu ione maliseche ako,Ndipo maufumu adzaona kuti wachititsidwa manyazi.