Nahumu 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kodi iwe uli pabwino kuposa No-amoni*+ amene anali pafupi ndi ngalande zochokera mumtsinje wa Nailo?+ Iye anazunguliridwa ndi madzi.Nyanja inali chuma chake ndiponso khoma lake. Nahumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:8 Nsanja ya Olonda,5/15/1989, ptsa. 24-25
8 Kodi iwe uli pabwino kuposa No-amoni*+ amene anali pafupi ndi ngalande zochokera mumtsinje wa Nailo?+ Iye anazunguliridwa ndi madzi.Nyanja inali chuma chake ndiponso khoma lake.