Nahumu 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mphamvu zake zopanda malire zinkachokera ku Itiyopiya ndi ku Iguputo. Anthu a ku Puti+ ndi a ku Libiya ankamuthandiza.+
9 Mphamvu zake zopanda malire zinkachokera ku Itiyopiya ndi ku Iguputo. Anthu a ku Puti+ ndi a ku Libiya ankamuthandiza.+