-
Nahumu 3:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Malo ako onse okhala ndi mipanda yolimba ali ngati mitengo ya mkuyu yokhala ndi nkhuyu zoyambirira kupsa.
Munthu akagwedeza mitengoyo, nkhuyu zakezo zimagwera mʼkamwa mwa munthu wozidya.
-