-
Nahumu 3:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Taona! Asilikali ako ali ngati akazi.
Mageti a dziko lako adzatsegulidwa kuti adani ako alowemo.
Ndipo moto udzawotcheratu mipiringidzo ya mageti ako.
-