Nahumu 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tunga madzi pokonzekera nthawi imene adani adzakuzungulire.+ Limbitsa malo ako okhala ndi mipanda yolimba. Lowa mʼmatope ndi kupondaponda dothi.Gwira chikombole.
14 Tunga madzi pokonzekera nthawi imene adani adzakuzungulire.+ Limbitsa malo ako okhala ndi mipanda yolimba. Lowa mʼmatope ndi kupondaponda dothi.Gwira chikombole.