-
Nahumu 3:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Alonda ako ali ngati dzombe.
Ndipo akapitawo ako ali ngati gulu la dzombe.
Pa tsiku lozizira limakhala mʼmakoma.
Koma dzuwa likawala, dzombelo limauluka nʼkupita kutali.
Ndipo palibe amene amadziwa kumene lapita.
-