Nahumu 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Abusa ako ayamba kuodzera, iwe mfumu ya Asuri,Ndipo anthu ako olemekezeka akungokhala mʼnyumba zawo. Anthu ako amwazikana mʼmapiri,Ndipo palibe amene akuwasonkhanitsa.+
18 Abusa ako ayamba kuodzera, iwe mfumu ya Asuri,Ndipo anthu ako olemekezeka akungokhala mʼnyumba zawo. Anthu ako amwazikana mʼmapiri,Ndipo palibe amene akuwasonkhanitsa.+