-
Habakuku 1:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Nʼchifukwa chiyani mukundichititsa kuona zinthu zoipa?
Nʼchifukwa chiyani mukulekerera kuponderezana?
Nʼchifukwa chiyani kuwononga zinthu komanso chiwawa zikuchitika pamaso panga?
Ndipo nʼchifukwa chiyani mikangano ndi kumenyana zachuluka?
-