Habakuku 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho lamulo latha mphamvu,Ndipo anthu sakuchitanso chilungamo. Oipa akupondereza anthu olungama,Nʼchifukwa chake chilungamo chikupotozedwa.+ Habakuku Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:4 Nsanja ya Olonda,2/1/2000, tsa. 9
4 Choncho lamulo latha mphamvu,Ndipo anthu sakuchitanso chilungamo. Oipa akupondereza anthu olungama,Nʼchifukwa chake chilungamo chikupotozedwa.+