Habakuku 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Maso anu ndi oyera kwambiri moti simungaonerere zinthu zoipa,Ndipo simungalekerere khalidwe loipa.+ Ndiye nʼchifukwa chiyani mukulekerera anthu achinyengo,+Komanso mukukhala chete pamene munthu woipa akumeza munthu wolungama kuposa iyeyo?+ Habakuku Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:13 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2018, tsa. 15 Nsanja ya Olonda,2/1/2000, tsa. 129/15/1989, ptsa. 17-18
13 Maso anu ndi oyera kwambiri moti simungaonerere zinthu zoipa,Ndipo simungalekerere khalidwe loipa.+ Ndiye nʼchifukwa chiyani mukulekerera anthu achinyengo,+Komanso mukukhala chete pamene munthu woipa akumeza munthu wolungama kuposa iyeyo?+
1:13 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2018, tsa. 15 Nsanja ya Olonda,2/1/2000, tsa. 129/15/1989, ptsa. 17-18