Habakuku 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye* amakola zonsezi ndi mbedza, Ndipo amazikokolola ndi khoka lake.Nʼkuzisonkhanitsa muukonde wophera nsomba. Nʼchifukwa chake iye amasangalala kwambiri.+
15 Iye* amakola zonsezi ndi mbedza, Ndipo amazikokolola ndi khoka lake.Nʼkuzisonkhanitsa muukonde wophera nsomba. Nʼchifukwa chake iye amasangalala kwambiri.+