Habakuku 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Nʼchifukwa chake amapereka nsembe kwa khoka lake,Ndipo amapereka nsembe yautsi kwa ukonde wake wophera nsomba.Iye amatero chifukwa khoka ndi ukondewo zimamuthandiza kupeza chakudya chambiri.*Ndipo chakudya chake ndi chapamwamba.
16 Nʼchifukwa chake amapereka nsembe kwa khoka lake,Ndipo amapereka nsembe yautsi kwa ukonde wake wophera nsomba.Iye amatero chifukwa khoka ndi ukondewo zimamuthandiza kupeza chakudya chambiri.*Ndipo chakudya chake ndi chapamwamba.