Habakuku 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako Yehova anandiyankha kuti: “Lemba masomphenyawa mooneka bwino pamiyala yosema,+Kuti wowerenga mokweza asavutike kuwerenga.*+ Habakuku Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:2 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2018, ptsa. 13-14
2 Kenako Yehova anandiyankha kuti: “Lemba masomphenyawa mooneka bwino pamiyala yosema,+Kuti wowerenga mokweza asavutike kuwerenga.*+