-
Habakuku 2:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Tsoka kwa munthu amene akupezera nyumba yake phindu mwachinyengo,
Kuti amange chisa chake pamwamba,
Nʼcholinga choti tsoka lisamupeze.
-