-
Habakuku 2:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Tsoka kwa amene amapatsa anzake chakumwa,
Atasakanizamo mkwiyo ndi kupsa mtima kuti anzakewo aledzere,
Nʼcholinga choti aone maliseche awo.
-