Habakuku 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Inu Yehova, ndamva uthenga wonena za inu. Ndachita mantha ndi ntchito zanu, inu Yehova. Mʼzaka zimenezi* sonyezani ntchito zanu. Mʼzaka zimenezi chititsani kuti ntchito zanu zidziwike. Pa nthawi ya mkwiyo wanu kumbukirani kusonyeza chifundo.+ Habakuku Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:2 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 108-109 Nsanja ya Olonda,2/1/2000, tsa. 20
2 “Inu Yehova, ndamva uthenga wonena za inu. Ndachita mantha ndi ntchito zanu, inu Yehova. Mʼzaka zimenezi* sonyezani ntchito zanu. Mʼzaka zimenezi chititsani kuti ntchito zanu zidziwike. Pa nthawi ya mkwiyo wanu kumbukirani kusonyeza chifundo.+