Habakuku 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye anaimirira nʼkugwedeza dziko lapansi.+ Atayangʼana mitundu ya anthu, mitunduyo inadumpha.+ Mapiri akuluakulu omwe adzakhalapo mpaka kalekale anaphwanyidwa,Ndipo mapiri angʼonoangʼono akalekale anawerama.+ Njira zakalekale ndi zake. Habakuku Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:6 Nsanja ya Olonda,11/15/2007, tsa. 102/1/2000, tsa. 21 Tsiku la Yehova, tsa. 32 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 108-109
6 Iye anaimirira nʼkugwedeza dziko lapansi.+ Atayangʼana mitundu ya anthu, mitunduyo inadumpha.+ Mapiri akuluakulu omwe adzakhalapo mpaka kalekale anaphwanyidwa,Ndipo mapiri angʼonoangʼono akalekale anawerama.+ Njira zakalekale ndi zake.
3:6 Nsanja ya Olonda,11/15/2007, tsa. 102/1/2000, tsa. 21 Tsiku la Yehova, tsa. 32 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 108-109