Habakuku 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu Yehova, kodi mwapsera mtima mitsinje?Kapena kodi mwakwiyira kwambiri nyanja?+ Chifukwa munakwera pamahatchi anu,+ Magaleta anu anapambana.+
8 Inu Yehova, kodi mwapsera mtima mitsinje?Kapena kodi mwakwiyira kwambiri nyanja?+ Chifukwa munakwera pamahatchi anu,+ Magaleta anu anapambana.+