Habakuku 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mapiri atakuonani anamva ululu waukulu.+ Mvula yamphamvu inadutsa. Madzi akuya anachita mkokomo,+ Ndipo anathovokera mʼmwamba. Habakuku Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:10 Nsanja ya Olonda,2/1/2000, ptsa. 21-22 Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 156-157
10 Mapiri atakuonani anamva ululu waukulu.+ Mvula yamphamvu inadutsa. Madzi akuya anachita mkokomo,+ Ndipo anathovokera mʼmwamba.