-
Habakuku 3:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Munapita kukapulumutsa anthu anu, kuti mupulumutse wodzozedwa wanu.
Munaphwanyaphwanya mtsogoleri wa nyumba ya ochimwa.
Nyumba yonseyo inagumulidwa mpaka maziko ake anaonekera. (Selah)
-