Habakuku 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Munabaya mitu ya asilikali ake pogwiritsa ntchito zida* zake zomwe,Pamene iwo ankabwera ngati mphepo yamkuntho kuti adzandiuluze, Anasangalala kwambiri kumeza munthu wosautsidwa amene anamubisalira. Habakuku Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:14 Nsanja ya Olonda,2/1/2000, ptsa. 22-23
14 Munabaya mitu ya asilikali ake pogwiritsa ntchito zida* zake zomwe,Pamene iwo ankabwera ngati mphepo yamkuntho kuti adzandiuluze, Anasangalala kwambiri kumeza munthu wosautsidwa amene anamubisalira.