Zefaniya 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Mʼmasiku a Yosiya+ mwana wa Amoni+ mfumu ya Yuda, Yehova analankhula kudzera mwa Zefaniya* mwana wa Kusa, mwana wa Gedaliya, mwana wa Amariya, mwana wa Hezekiya. Iye anati: Zefaniya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:1 Nsanja ya Olonda,2/15/2001, tsa. 123/1/1996, tsa. 8
1 Mʼmasiku a Yosiya+ mwana wa Amoni+ mfumu ya Yuda, Yehova analankhula kudzera mwa Zefaniya* mwana wa Kusa, mwana wa Gedaliya, mwana wa Amariya, mwana wa Hezekiya. Iye anati: