Zefaniya 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Ndidzasesa anthu ndi nyama. Ndidzasesa mbalame zamumlengalenga ndiponso nsomba zamʼnyanja.+Ndidzasesanso zopunthwitsa*+ pamodzi ndi anthu oipa,Ndipo ndidzawononga anthu onse padziko,” watero Yehova. Zefaniya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:3 Nsanja ya Olonda,2/15/2001, ptsa. 12-13
3 “Ndidzasesa anthu ndi nyama. Ndidzasesa mbalame zamumlengalenga ndiponso nsomba zamʼnyanja.+Ndidzasesanso zopunthwitsa*+ pamodzi ndi anthu oipa,Ndipo ndidzawononga anthu onse padziko,” watero Yehova.