Zefaniya 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Ndidzatambasula dzanja langa nʼkuwononga Yuda,Ndiponso anthu onse okhala mu Yerusalemu.Ndidzawononga chilichonse chokhudza Baala+ pamalowa.Ndidzawononganso ansembe komanso dzina la ansembe a mulungu wachilendo.+ Zefaniya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:4 Nsanja ya Olonda,2/15/2001, ptsa. 13, 173/1/1996, ptsa. 9, 13-14
4 “Ndidzatambasula dzanja langa nʼkuwononga Yuda,Ndiponso anthu onse okhala mu Yerusalemu.Ndidzawononga chilichonse chokhudza Baala+ pamalowa.Ndidzawononganso ansembe komanso dzina la ansembe a mulungu wachilendo.+ Zefaniya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:4 Nsanja ya Olonda,2/15/2001, ptsa. 13, 173/1/1996, ptsa. 9, 13-14