Zefaniya 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Khalani chete pamaso pa Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, chifukwa tsiku la Yehova lili pafupi,+ Yehova wakonza nsembe ndipo wayeretsa anthu amene wawaitana. Zefaniya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:7 Nsanja ya Olonda,2/15/2001, ptsa. 13-14
7 Khalani chete pamaso pa Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, chifukwa tsiku la Yehova lili pafupi,+ Yehova wakonza nsembe ndipo wayeretsa anthu amene wawaitana.