-
Zefaniya 1:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Pa tsiku limenelo ndidzaweruza aliyense amene amakwera pamalo omwe pamakhala mpando wachifumu,
Anthu amene adzaza nyumba ya ambuye awo ndi chiwawa ndiponso chinyengo.”
-