Zefaniya 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yehova wanena kuti: “Patsiku limenelo,Ku Geti la Nsomba+ kudzamveka phokoso la anthu,Ndipo Kumbali Yatsopano ya mzinda kudzamveka kulira mokweza.+Kumapiri kudzamveka phokoso la chiwonongeko. Zefaniya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:10 Nsanja ya Olonda,2/15/2001, tsa. 143/1/1996, ptsa. 10-11
10 Yehova wanena kuti: “Patsiku limenelo,Ku Geti la Nsomba+ kudzamveka phokoso la anthu,Ndipo Kumbali Yatsopano ya mzinda kudzamveka kulira mokweza.+Kumapiri kudzamveka phokoso la chiwonongeko.