Zefaniya 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chuma chawo chidzatengedwa ndipo nyumba zawo zidzawonongedwa.+ Iwo adzamanga nyumba, koma sadzakhalamo.Iwo adzalima minda ya mpesa koma sadzamwa vinyo wake.+ Zefaniya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:13 Nsanja ya Olonda,2/15/2001, ptsa. 14-153/1/1996, ptsa. 9, 16-17
13 Chuma chawo chidzatengedwa ndipo nyumba zawo zidzawonongedwa.+ Iwo adzamanga nyumba, koma sadzakhalamo.Iwo adzalima minda ya mpesa koma sadzamwa vinyo wake.+