Zefaniya 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsiku loliza lipenga ndiponso la mfuu yankhondo,+Pochenjeza mizinda ya mipanda yolimba komanso nsanja zazitali zamʼmakona.+ Zefaniya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:16 Nsanja ya Olonda,2/15/2001, ptsa. 15-16
16 Tsiku loliza lipenga ndiponso la mfuu yankhondo,+Pochenjeza mizinda ya mipanda yolimba komanso nsanja zazitali zamʼmakona.+