Zefaniya 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Siliva kapena golide wawo sadzawapulumutsa pa tsiku la mkwiyo wa Yehova.+Popeza moto wa mkwiyo wake udzawotcheratu dziko lonse lapansi,+Chifukwa iye adzawononga anthu onse apadziko lapansi.”+ Zefaniya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:18 Nsanja ya Olonda,2/15/2001, ptsa. 16-173/1/1996, tsa. 14
18 Siliva kapena golide wawo sadzawapulumutsa pa tsiku la mkwiyo wa Yehova.+Popeza moto wa mkwiyo wake udzawotcheratu dziko lonse lapansi,+Chifukwa iye adzawononga anthu onse apadziko lapansi.”+