Zefaniya 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anthu amenewo adzaona zimenezi chifukwa cha kunyada kwawo,+Chifukwa ankanyoza anthu a Yehova wa magulu ankhondo akumwamba ndipo ankadzikweza pamaso pawo.
10 Anthu amenewo adzaona zimenezi chifukwa cha kunyada kwawo,+Chifukwa ankanyoza anthu a Yehova wa magulu ankhondo akumwamba ndipo ankadzikweza pamaso pawo.