-
Zefaniya 2:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Magulu a nyama kapena kuti nyama zakutchire za mitundu yonse zidzagona mumzindawo.
Nungu ndiponso mbalame ya vuwo zidzagona usiku wonse pamitu ya zipilala zamzindawo.
Pawindo padzamveka nyimbo.
Pamakomo a nyumba padzakhala zibulumwa za nyumba zakugwa,
Chifukwa iye adzachititsa kuti matabwa oyalidwa kukhoma akhale pamtunda.
-