Zefaniya 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Akalonga ake ali ngati mikango yobangula.+ Oweruza ake ali ngati mimbulu imene ikuyenda usiku.Imene pofika mʼmawa imadya chilichonse osasiya ngakhale fupa. Zefaniya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:3 Tsiku la Yehova, tsa. 78 Nsanja ya Olonda,3/1/1996, ptsa. 9, 145/1/1991, ptsa. 19-20
3 Akalonga ake ali ngati mikango yobangula.+ Oweruza ake ali ngati mimbulu imene ikuyenda usiku.Imene pofika mʼmawa imadya chilichonse osasiya ngakhale fupa.