Zefaniya 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Ine ndinawononga mitundu ya anthu ndi kusakaza nsanja zawo zamʼmakona. Ndinawononga misewu yawo moti simunkayendanso anthu. Mizinda yawo inakhala mabwinja ndipo simunatsale munthu aliyense.+ Zefaniya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:6 Nsanja ya Olonda,2/15/2001, tsa. 22
6 “Ine ndinawononga mitundu ya anthu ndi kusakaza nsanja zawo zamʼmakona. Ndinawononga misewu yawo moti simunkayendanso anthu. Mizinda yawo inakhala mabwinja ndipo simunatsale munthu aliyense.+