Zefaniya 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndidzasiya anthu odzichepetsa ndi ofatsa kuti akhalebe pakati panu,+Ndipo iwo adzapeza chitetezo mʼdzina la Yehova. Zefaniya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:12 Nsanja ya Olonda,1/15/2011, tsa. 52/15/2001, tsa. 243/1/1996, tsa. 14
12 Ndidzasiya anthu odzichepetsa ndi ofatsa kuti akhalebe pakati panu,+Ndipo iwo adzapeza chitetezo mʼdzina la Yehova.