Zefaniya 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Aisiraeli otsala+ sadzachita zinthu zosalungama.+Sadzalankhula bodza kapena kukhala ndi lilime lachinyengo.Iwo adzadya ndi kugona ndipo sipadzakhala wowaopseza.”+ Zefaniya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:13 Nsanja ya Olonda,2/15/2001, tsa. 243/1/1996, tsa. 14
13 Aisiraeli otsala+ sadzachita zinthu zosalungama.+Sadzalankhula bodza kapena kukhala ndi lilime lachinyengo.Iwo adzadya ndi kugona ndipo sipadzakhala wowaopseza.”+