Zefaniya 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yehova Mulungu wako ali pakati panu+ Ndipo adzakupulumutsa chifukwa ndi wamphamvu. Iye adzakondwera nawe.+ Adzakhala phee chifukwa chokhutira ndi chikondi chimene akukusonyeza, Ndipo adzafuula mosangalala chifukwa chokondwera nawe. Zefaniya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:17 Nsanja ya Olonda,1/15/2011, tsa. 52/15/2001, tsa. 263/1/1996, ptsa. 16, 17-18
17 Yehova Mulungu wako ali pakati panu+ Ndipo adzakupulumutsa chifukwa ndi wamphamvu. Iye adzakondwera nawe.+ Adzakhala phee chifukwa chokhutira ndi chikondi chimene akukusonyeza, Ndipo adzafuula mosangalala chifukwa chokondwera nawe.