Zefaniya 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pa nthawiyo ndidzalanga onse amene akukupondereza,+Ndipo ndidzapulumutsa wotsimphina.+Ndidzasonkhanitsa anthu amene anabalalitsidwa.+ Ndidzachititsa kuti akhale otchuka* komanso azitamandidwa,Mʼdziko lonse limene anachititsidwa manyazi.
19 Pa nthawiyo ndidzalanga onse amene akukupondereza,+Ndipo ndidzapulumutsa wotsimphina.+Ndidzasonkhanitsa anthu amene anabalalitsidwa.+ Ndidzachititsa kuti akhale otchuka* komanso azitamandidwa,Mʼdziko lonse limene anachititsidwa manyazi.