Hagai 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mwadzala mbewu zambiri, koma mukukolola zochepa.+ Mukudya, koma simukukhuta. Mukumwa koma simukukhutira. Mukuvala zovala, koma simukumva kutenthera. Ndipo amene akugwira ganyu akuika ndalama zake mʼmatumba obowoka.’” Hagai Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:6 Nsanja ya Olonda,12/1/2007, tsa. 94/15/2006, tsa. 226/1/1989, tsa. 30
6 Mwadzala mbewu zambiri, koma mukukolola zochepa.+ Mukudya, koma simukukhuta. Mukumwa koma simukukhutira. Mukuvala zovala, koma simukumva kutenthera. Ndipo amene akugwira ganyu akuika ndalama zake mʼmatumba obowoka.’”