Hagai 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 ‘Pitani kuphiri mukatenge mitengo yomangira nyumba.+ Mumange nyumbayi+ kuti ndisangalale nayo komanso kuti nditamandidwe,’+ watero Yehova.”
8 ‘Pitani kuphiri mukatenge mitengo yomangira nyumba.+ Mumange nyumbayi+ kuti ndisangalale nayo komanso kuti nditamandidwe,’+ watero Yehova.”