-
Hagai 1:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 “‘Munkayembekezera zinthu zambiri, koma mwapeza zochepa. Mutabweretsa zinthuzo mʼnyumba zanu, ine ndaziuzira nʼkuzimwaza.+ Nʼchifukwa chiyani ndachita zimenezi? Chifukwa nyumba yanga ili ngati bwinja, pomwe aliyense wa inu akuthamangathamanga kuti asamalire nyumba yake,’+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.
-